Luka 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali tsiku la Sabata, iye analinkupita pakati pa minda ya tirigu; ndipo ophunzira ace analinkubudula ngala za tirigu, nazifikisa m'manja mwao, nadya.

Luka 6

Luka 6:1-8