Luka 5:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Simoni Petro, pamene anaona, anagwa pansi pa mabondo ace a Yesu, nanena, Mucoke kwa ine, Ambuye, cifukwa ndine munthu wocimwa.

Luka 5

Luka 5:7-12