Luka 5:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo palibe munthu atsanulira vinyo watsopano m'matumba akale; cifukwa ngati atero, vinyo watsopanoyo adzaphulitsa matumba, ndipo ameneyo adzatayika, ndi matumba adzaonongeka.

Luka 5

Luka 5:33-39