Luka 5:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anati kwa iye, Ophunzira a Yohane amasala kudya kawiri kawiri, ndi kucita mapemphero; cimodzimodzinso iwo a Afarisi; koma anu amangokudya ndi kumwa.

Luka 5

Luka 5:23-39