Luka 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mdierekezi anati kwa iye, Ine ndidzapatsa Inu ulamuliro wonse umenewu ndi ulemerero wao: cifukwa unaperekedwa kwa ine; ndipo ndiupatsa kwa iye amene ndifuna.

Luka 4

Luka 4:1-7