Luka 4:43-44 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

43. Koma anati kwa iwo, Kundiyenera Ine ndilalikire Uthenga Wabwino wa Ufumu wa Mulungu ku midzi yinanso: cifukwa ndinatumidwa kudzatero.

44. Ndipo iye analikulalikira m'masunagoge a ku Galileya.

Luka 4