Luka 4:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kutaca anaturuka iye nanka ku malo acipululu; ndi makamu a anthu analikwnfunafuna iye, nadza nafika kwa iye, nayesa kumletsa iye, kuti asawacokere.

Luka 4

Luka 4:32-44