Luka 4:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse anadabwa, nalankhulana wina ndi mnzace, nanena, Mau amenewa ali otani? cifukwa ndi ulamuliro ndi mphamvu angolamulira mizimu yonyansa, ndipo ingoturuka.

Luka 4

Luka 4:34-42