Luka 3:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

monga mwalembedwa m'kalata wa mau a Yesaya mneneri, kuti,Mau a wopfuula m'cipululu,Konzani khwalala la Ambuye,Lungamitsani njira zace.

Luka 3

Luka 3:1-14