Luka 3:23-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Ndipo Yesuyo, pamene anayamba nchito yace, anali monga wa zaka makumi atatu, ndiye (monga anthu adamuyesa) mwana wa Yosefe, mwana wa Heli,

24. mwana wa Matati, mwana wa Levi, mwana wa Melki, mwana wa Yanai, mwana wa Yosefe,

25. mwana wa Matatio, mwana wa Amosi, mwana wa Naumi, mwana wa Esli, mwana wa Nagai,

26. mwana wa Maati, mwana wa Matatio, mwana wa Semeini, mwana wa Yosefe, mwana wa Yoda,

Luka 3