Luka 24:52-53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

52. Ndipo 14 anamlambira iye, nabwera ku Yerusalemu ndi cimwemwe cacikuru;

53. ndipo IS anakhala ci khalire m'Kacisi, nalikuyamika Mulungu, Amen.

Luka 24