Luka 24:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Penyani manja anga ndi mapazianga, kuti Ine ndine mwini: 2 ndikhudzeni, ndipo penyani; pakuti mzimu ulibe, mnofu ndi mafupa, monga muona ndirinazo Ine.

Luka 24

Luka 24:34-47