Luka 24:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndipo m'mene analowa sanapeza mtembo wa Ambuye Yesu.

4. Ndipo kunali, m'mene anathedwa nzeru naco, taonani amuna awiri anaimirira pafupi pao atabvala zonyezimira;

5. ndipo m'mene anakhala ndi mantha naweramira pansi nkhope zao, anati kwa iwo, Mufuniranji wamoyo pa akufa?

Luka 24