Luka 24:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, awiri a mwa iwo analikupita tsiku lomwelo kumudzi dzina lace Emau, wosiyana ndi Yerusalemu mastadiya makumi asanu ndi limodzi.

Luka 24

Luka 24:12-23