Luka 24:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma tsiku loyamba la sabata, mbanda kuca, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza.

2. Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuucotsa pamanda.

Luka 24