Luka 23:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Yesu anapfuula ndi mau akuru, anati, 1 Atate, m'manja mwanu ndipereka mzimu wanga. Ndipo pakutero anapereka mzimu wace.

Luka 23

Luka 23:40-47