Luka 23:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu ananena, Atate, muwakhululukire iwo, pakuti sadziwa cimene acita. Ndipo anagawana zobvala zace, poyesa maere.

Luka 23

Luka 23:29-41