Luka 23:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo popita naye, anagwira munthu, Simoni wa ku Kurene, alikucokera kuminda, namsenza iye mtanda aunyamule pambuyo pace pa Yesu,

Luka 23

Luka 23:17-27