Luka 22:61 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ambuye anapotoloka, nayang'ana Petro. Ndipo 11 Petra anakumbukila mau a Ambuye, kuti anati kwa iye, 12 Asanalire tambala lero lino, udzandikana Ine katatu.

Luka 22

Luka 22:53-70