Luka 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati kwa iwo, Onani, mutalowa m'mudzi, adzakomana ndinu munthu alikusenza mtsuko wa madzi; mumtsate ameneyo kunyumba kumene akalowako iye.

Luka 22

Luka 22:4-12