Luka 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti onse amenewa anaika mwa unyinji wao pa zoperekazo; koma iye mwa kusowa kwace anaikamo za moyo wace, zonse anali nazo.

Luka 21

Luka 21:1-14