Luka 21:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo usana uli wonse iye analikuphunzitsa m'Kacisi; ndi usiku uli wonse anaturuka, nagona pa phiri lochedwa la Azitona.

Luka 21

Luka 21:27-38