1. Ndipo Yesu anakweza maso, naona anthu eni cuma alikuika zopereka zao mosungiramo ndalama.
2. Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri.
3. Ndipo iye anati, Zoonadi ndinena kwa inu, wamasiye uyu waumphawi anaikamo koposa onse;