Luka 20:38-41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Ndipo iye sakhala Mulungu wa akufa, koma wa amoyo: pakuti anthu onse akhala ndi moyo kwa iye.

39. Ndipo alembi ena anayankha nati, Mphunzitsi, mwanena bwino.

40. Pakuti sanalimbanso mtima kumfunsa iye kanthu kena.

41. Koma iye anati kwa iwo, Amanena bwanji kuti Kristuyo ndiye mwana wa Davine?

Luka 20