Luka 20:31-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. ndi wacitatu anamtenga mkaziyo; ndipo coteronso asanu ndi awiri onse, sanasiya mwana, namwalira.

32. Pomarizira anamwaliranso mkaziyo.

33. Potero m'kuuka iye adzakhala mkazi wa yani wa iwo? pakuti asanu ndi awiriwo adamkwatira iye.

34. Ndipo Yesu anati kwa iwo, Ana a dziko lapansi akwatira nakwatiwa:

Luka 20