Luka 20:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndipo anayankha, nati kwa iwo, Ndidzakufunsani mau Inenso; mundiuze:

4. Ubatizo wa Yohane unacokera Kumwamba kodi, kapena kwa anthu?

5. Ndipo anatsutsana mwa okha, nanena, Ngati tinena ucokera Kumwamba; adzati, Simunamkhulupirira cifukwa ninji?

Luka 20