Luka 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pa nyengo ya zipatso anatumiza kapolo wace kwa olima mundawo, kuti ampatseko cipatso ca mundawo; koma olimawo anampanda, nambweza wopanda kanthu.

Luka 20

Luka 20:3-13