Luka 2:50-52 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

50. Ndipo 6 sanadziwitsa mau amene iye analankhula nao.

51. Ndipo anatsika nao pamodzi nadza ku Nazarete; nawamvera iwo: ndipo 7 amace anasunga zinthu izi zonse mumtima mwace.

52. Ndipo Yesu 8 anakulabe m'nzeru ndi mumsinkhu, ndi m'cisomo ca pa Mulungu ndi ca pa anthu.

Luka 2