Luka 2:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakupita masiku atatu, anampeza iye m'Kacisi, analikukhala pakati pa aphunzitsi, namva iwo, nawafunsanso mafunso.

Luka 2

Luka 2:43-52