Luka 2:29-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Tsopano, Ambuye, monga mwa mau anu aja,Lolani ine, kapolo wanu, ndicoke mumtendere;

30. Cifukwa maso anga adaona cipulumutso canu,

31. Cimene munakonza pamaso pa anthu onse,

32. Kuunika kukhale cibvumbulutso ca kwa anthu a mitundu,Ndi ulemerero wa anthu anu Israyeli.

Luka 2