Luka 2:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anakwanira masiku a kukonza kwao, monga mwa cilamulo ca Mose, iwo anakwera naye kunka ku Yerusalemu, kukamsonyeza iye kwa Ambuye,

Luka 2

Luka 2:12-30