Luka 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo abusawo anabwera, nalemekeza ndi kutamanda Mulungu pa zinthu zonse anazimva, naziona, monga kunalankhulidwa kwa iwo.

Luka 2

Luka 2:10-24