Luka 2:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mngelo anati kwa iwo, Musaope; pakuti onani, ndikuuzani inu uthenga wabwino wa cikondwero cacikuru, cimene cidzakhala kwa anthu onse;

Luka 2

Luka 2:6-18