Luka 19:47-48 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

47. Ndipo analikuphunzitsa m'Kacisi tsiku ndi tsiku. Koma ansembe akulu, ndi alembi ndi akulu a anthu anafunafuna kumuononga iye;

48. ndipo sanapeza cimene akacita; pakuti anthu onse anamlendewera iye kuti amve.

Luka 19