Luka 19:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anati kwa iye, Cabwino, kapolo wabwino iwe; popeza unakhala wokhulupirika m'cacing'onong'ono, khala nao ulamuliro pa midzi khumi.

Luka 19

Luka 19:8-22