Luka 19:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakubwera iye, atalandira ufumuwo, anati aitanidwe kwa iye akapolo aja, amene adawapatsa ndalamazo, kuti adziwe umo anapindulira pocita malonda.

Luka 19

Luka 19:11-20