Luka 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakumva izi iwo, iye anaonjeza nanena fanizo, cifukwa anali iye pafupi pa Yerusalemu, ndipo iwo anayesa kuti Ufumu wa Mulungu ukuti uonekere pomwepo.

Luka 19

Luka 19:6-15