Luka 18:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadzitengera khumi ndi awiriwo, nati kwa iwo, Taonani, tikwera kunkaku Yerusalemu, ndipo zidzakwaniritsidwa kwa Mwana wa munthu zonse zolembedwa ndi aneneri.

Luka 18

Luka 18:26-40