Luka 18:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Palibe munthu wasiya nyumba, kapena mkazi, kapena abale, kapena akumbala, kapena ana, cifukwa ca Ufumu wa Mulungu,

Luka 18

Luka 18:21-31