Luka 18:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wamsonkhoyo alikuima patali sanafuna kungakhale kukweza maso kumwamba, komatu anadziguguda pacifuwa pace nanena, Mulungu, mundicitire cifundo, ine wocimwa.

Luka 18

Luka 18:9-17