Luka 17:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Ambuye anati, Mukakhala naco cikhulupiriro ngati kambeu kampiru, mukanena kwa mtengo uwu wamkuyu, Uzulidwe, nuokedwe m'nyanja; ndipo ukadamvera inu.

Luka 17

Luka 17:1-13