Luka 17:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akakucimwira kasanu ndi kawiri pa tsiku lace, nakakutembenukira kasanu ndi kawiri ndi kunena, Ndalapa ine; uzimkhululukira.

Luka 17

Luka 17:1-11