Luka 17:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakuwaona anati kwa iwo, Pitani, kadzionetseni nokha kwa ansembe. Ndipo kunali, m'kumuka kwao, anakonzedwa.

Luka 17

Luka 17:5-21