Luka 16:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Ine ndinena kwa inu, Mudziyesere nokha abwenzi ndi cuma cosalungama; kuti pamene cikakusowani, iwo akalandire inu m'mahema osatha.

Luka 16

Luka 16:5-12