Luka 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo anati kwa wina, Ndipo iwe uli nao mangawa otani? Ndipo uyu anati, Mitanga ya tirigu zana iye ananena naye, Tenga kalata wako nulembere makumi asanu ndi atatu.

Luka 16

Luka 16:1-16