Luka 15:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye ananyamuka, nadza kwa atate wace. Koma pakudza iye kutali, atate wace anamuona, nagwidwa cifundo, nathamanga, namkupatira pakhosi pace, nampsompsonetsa.

Luka 15

Luka 15:17-30