Luka 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakupita masiku owerengekamwana wamng'onoyo anasonkhanitsa zonse, napita ulendo wace ku dziko lakutari; ndipo komweko anamwaza cuma cace ndi makhalidwe a citayiko.

Luka 15

Luka 15:4-17