Luka 15:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco, ndinena kwa inu, kuli cimwemwe pamaso pa angelo a Mulungu cifukwa ca munthu wocimwa mmodzi amene atembenuka mtima.

Luka 15

Luka 15:1-12