Luka 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munthu akadza kwa Ine, wosada atate wace ndi amace, ndi mkazi wace, ndi ana, ndi abale, ndi alongo ace, inde ndi moyo wace womwe wa iye mwini, sakhoza kukhala wophunzira wanga.

Luka 14

Luka 14:22-29