Luka 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse ndi mtima umodzi anayamba kuwiringula. Woyamba anati kwa iye, Ine ndagula munda, ndipo ndiyenera ndituruke kukauona; ndikupempha undilole ine ndisafika.

Luka 14

Luka 14:9-20